Numeri 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Lamula Aisiraeli kuti azitulutsa mumsasa munthu aliyense wakhate,+ aliyense wakukha kumaliseche+ komanso aliyense wodetsedwa chifukwa chokhudza munthu wakufa.+ Numeri 19:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Aliyense wokhudza mtembo wa munthu aliyense, azikhala wodetsedwa kwa masiku 7.+ Numeri 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Aliyense amene wakhudza munthu amene waphedwa ndi lupanga kunja kwa msasa, kapena mtembo, fupa la munthu, kapenanso manda, adzakhala wodetsedwa kwa masiku 7.+
2 “Lamula Aisiraeli kuti azitulutsa mumsasa munthu aliyense wakhate,+ aliyense wakukha kumaliseche+ komanso aliyense wodetsedwa chifukwa chokhudza munthu wakufa.+
16 Aliyense amene wakhudza munthu amene waphedwa ndi lupanga kunja kwa msasa, kapena mtembo, fupa la munthu, kapenanso manda, adzakhala wodetsedwa kwa masiku 7.+