Numeri 11:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Anthuwo atachoka pa Kibiroti-hatava, anasamukira ku Hazeroti,+ ndipo anakhala kumeneko. Numeri 12:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako anthuwo anachoka ku Hazeroti,+ nʼkukamanga msasa mʼchipululu cha Parana.+