Yoswa 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Dziko lanu lidzayambira kuchipululu kufika ku Lebanoni mpaka kumtsinje waukulu wa Firate, dziko lonse la Ahiti+ mpaka kukafika ku Nyanja Yaikulu* kumadzulo.+ Yoswa 15:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Malire akumadzulo anali Nyanja Yaikulu*+ ndi gombe lake. Amenewa anali malire a ana a Yuda a mbali zonse motsatira mabanja awo.
4 Dziko lanu lidzayambira kuchipululu kufika ku Lebanoni mpaka kumtsinje waukulu wa Firate, dziko lonse la Ahiti+ mpaka kukafika ku Nyanja Yaikulu* kumadzulo.+
12 Malire akumadzulo anali Nyanja Yaikulu*+ ndi gombe lake. Amenewa anali malire a ana a Yuda a mbali zonse motsatira mabanja awo.