Numeri 3:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Mkulu wa atsogoleri onse a Alevi anali Eleazara,+ mwana wa wansembe Aroni. Iye ndi amene ankayangʼanira anthu onse amene ankatumikira pamalo oyera. Numeri 20:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mʼphirimo, ukamuvule Aroni zovala zake zaunsembe,+ nʼkuveka mwana wake Eleazara+ ndipo Aroni akamwalira kumeneko.” Yoswa 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Aisiraeli anatenga cholowa chawo mʼdziko la Kanani. Wansembe Eliezara, Yoswa mwana wa Nuni ndi atsogoleri a mafuko a makolo a Aisiraeli ndi amene anawagawira cholowachi.+
32 Mkulu wa atsogoleri onse a Alevi anali Eleazara,+ mwana wa wansembe Aroni. Iye ndi amene ankayangʼanira anthu onse amene ankatumikira pamalo oyera.
26 Mʼphirimo, ukamuvule Aroni zovala zake zaunsembe,+ nʼkuveka mwana wake Eleazara+ ndipo Aroni akamwalira kumeneko.”
14 Aisiraeli anatenga cholowa chawo mʼdziko la Kanani. Wansembe Eliezara, Yoswa mwana wa Nuni ndi atsogoleri a mafuko a makolo a Aisiraeli ndi amene anawagawira cholowachi.+