Ekisodo 25:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mundipangire malo opatulika, ndipo ndidzakhala pakati panu.+ Levitiko 26:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ine ndidzayenda pakati panu ndipo ndidzakhala Mulungu wanu,+ inuyo mudzakhala anthu anga.+