Ekisodo 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Ndipatulireni* mwana aliyense wamwamuna woyamba kubadwa,* wa munthu ndi wa chiweto, pakati pa Aisiraeli. Ameneyu ndi wanga.”+ Numeri 18:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chamoyo chilichonse choyamba kubadwa+ chimene azipereka kwa Yehova, kaya ndi munthu kapena nyama, chizikhala chako. Komabe uzionetsetsa kuti wawombola mwana woyamba kubadwa wa munthu+ komanso mwana woyamba kubadwa wa nyama yodetsedwa.+
2 “Ndipatulireni* mwana aliyense wamwamuna woyamba kubadwa,* wa munthu ndi wa chiweto, pakati pa Aisiraeli. Ameneyu ndi wanga.”+
15 Chamoyo chilichonse choyamba kubadwa+ chimene azipereka kwa Yehova, kaya ndi munthu kapena nyama, chizikhala chako. Komabe uzionetsetsa kuti wawombola mwana woyamba kubadwa wa munthu+ komanso mwana woyamba kubadwa wa nyama yodetsedwa.+