Numeri 4:22, 23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Uwerenge ana onse a Gerisoni+ potengera nyumba za makolo awo komanso mabanja awo. 23 Muwerenge onse kuyambira azaka 30 mpaka 50, amene ali mʼgulu la anthu amene anasankhidwa kuti azigwira ntchito mʼchihema chokumanako.
22 “Uwerenge ana onse a Gerisoni+ potengera nyumba za makolo awo komanso mabanja awo. 23 Muwerenge onse kuyambira azaka 30 mpaka 50, amene ali mʼgulu la anthu amene anasankhidwa kuti azigwira ntchito mʼchihema chokumanako.