Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 10:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “Mukamabwera kuchihema chokumanako, iwe ndi ana ako musamamwe vinyo kapena zakumwa zina zoledzeretsa,+ kuti mungafe. Limeneli ndi lamulo ku mibadwo yanu yonse mpaka kalekale.

  • Amosi 2:11, 12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ndinachititsa ana anu ena kukhala aneneri.+

      Ndipo anyamata anu ena ndinawachititsa kukhala Anaziri.+

      Si choncho kodi, inu Aisiraeli?’ watero Yehova.

      12 ‘Koma inu munkapatsa Anaziri vinyo kuti amwe,+

      Ndipo aneneri munawalamula kuti: “Musamanenere.”+

  • Luka 1:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 chifukwa adzakhala wamkulu pamaso pa Yehova.*+ Koma asadzamwe vinyo ngakhale pangʼono kapena chakumwa chilichonse choledzeretsa+ ndipo adzadzazidwa ndi mzimu woyera asanabadwe nʼkomwe.*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena