Levitiko 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako Aroni anakweza manja ake nʼkuloza anthuwo ndipo anawadalitsa.+ Atatero anatsika kuguwa lansembe atamaliza kupereka nsembe yamachimo, nsembe yopsereza ndi nsembe zamgwirizano. Deuteronomo 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pa nthawi imeneyo, Yehova anapatula fuko la Levi+ kuti lizinyamula likasa la pangano la Yehova,+ liziima pamaso pa Yehova nʼkumamutumikira komanso kuti lizidalitsa anthu mʼdzina lake+ ngati mmene akuchitira mpaka lero.
22 Kenako Aroni anakweza manja ake nʼkuloza anthuwo ndipo anawadalitsa.+ Atatero anatsika kuguwa lansembe atamaliza kupereka nsembe yamachimo, nsembe yopsereza ndi nsembe zamgwirizano.
8 Pa nthawi imeneyo, Yehova anapatula fuko la Levi+ kuti lizinyamula likasa la pangano la Yehova,+ liziima pamaso pa Yehova nʼkumamutumikira komanso kuti lizidalitsa anthu mʼdzina lake+ ngati mmene akuchitira mpaka lero.