Deuteronomo 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Pa nthawi imeneyo, Yehova anapatula fuko la Levi+ kuti lizinyamula likasa la pangano la Yehova,+ liziima pamaso pa Yehova pom’tumikira,+ ndi kuti lizidalitsa m’dzina lake kufikira lero.+
8 “Pa nthawi imeneyo, Yehova anapatula fuko la Levi+ kuti lizinyamula likasa la pangano la Yehova,+ liziima pamaso pa Yehova pom’tumikira,+ ndi kuti lizidalitsa m’dzina lake kufikira lero.+