Salimo 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chifukwa inu Yehova mudzadalitsa aliyense wolungama.Mudzasangalala nawo ndipo mudzawateteza ndi chishango chachikulu.+ Salimo 67:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mulungu adzatidalitsa,Ndipo anthu onse apadziko lapansi adzamuopa.*+
12 Chifukwa inu Yehova mudzadalitsa aliyense wolungama.Mudzasangalala nawo ndipo mudzawateteza ndi chishango chachikulu.+