Numeri 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Amene azimanga msasa wawo kumʼmwera ndi gulu la mafuko atatu la Rubeni+ ndi magulu awo.* Mtsogoleri wa ana a Rubeni ndi Elizuri,+ mwana wa Sedeuri. Numeri 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako, gulu la mafuko atatu la ana a Rubeni linanyamuka potengera magulu awo.* Mtsogoleri wa gululi anali Elizuri,+ mwana wa Sedeuri.
10 Amene azimanga msasa wawo kumʼmwera ndi gulu la mafuko atatu la Rubeni+ ndi magulu awo.* Mtsogoleri wa ana a Rubeni ndi Elizuri,+ mwana wa Sedeuri.
18 Kenako, gulu la mafuko atatu la ana a Rubeni linanyamuka potengera magulu awo.* Mtsogoleri wa gululi anali Elizuri,+ mwana wa Sedeuri.