Numeri 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako pazibwera fuko la Gadi. Mtsogoleri wa ana a Gadi ndi Eliyasafu,+ mwana wa Reueli. Numeri 10:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mtsogoleri wa gulu la fuko la ana a Gadi anali Eliyasafu,+ mwana wa Deyueli.