Numeri 2:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pafupi ndi fuko limeneli pazibwera fuko la Aseri. Mtsogoleri wa ana a Aseri ndi Pagiyeli,+ mwana wa Okirani. Numeri 10:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mtsogoleri wa gulu la fuko la ana a Aseri anali Pagiyeli,+ mwana wa Okirani.
27 Pafupi ndi fuko limeneli pazibwera fuko la Aseri. Mtsogoleri wa ana a Aseri ndi Pagiyeli,+ mwana wa Okirani.