Numeri 1:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Alevi azimanga matenti awo mozungulira chihema cha Umboni kuti mkwiyo wa Mulungu usayakire Aisiraeli.+ Aleviwo ndi amene ali ndi udindo wosamalira* chihema cha Umbonicho.”+ Numeri 18:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Inu nokha ndi amene muzigwira ntchito za ansembe mʼmalo opatulika+ ndi paguwa lansembe,+ kuti ndisadzakwiyirenso+ Aisiraeli. 1 Samueli 6:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma Mulungu anapha anthu a ku Beti-semesi chifukwa anayangʼana Likasa la Yehova. Anapha anthu 50,070* ndipo anthu anayamba kulira chifukwa Yehova anapha anthu ambiri.+
53 Alevi azimanga matenti awo mozungulira chihema cha Umboni kuti mkwiyo wa Mulungu usayakire Aisiraeli.+ Aleviwo ndi amene ali ndi udindo wosamalira* chihema cha Umbonicho.”+
5 Inu nokha ndi amene muzigwira ntchito za ansembe mʼmalo opatulika+ ndi paguwa lansembe,+ kuti ndisadzakwiyirenso+ Aisiraeli.
19 Koma Mulungu anapha anthu a ku Beti-semesi chifukwa anayangʼana Likasa la Yehova. Anapha anthu 50,070* ndipo anthu anayamba kulira chifukwa Yehova anapha anthu ambiri.+