Numeri 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano mʼchaka chachiwiri, mwezi wachiwiri, pa tsiku la 20 la mweziwo,+ mtambo uja unanyamuka pamwamba pa chihema+ cha Umboni. Numeri 10:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Akanyamuka pamsasa masana, mtambo wa Yehova+ unkakhala pamwamba pawo.
11 Tsopano mʼchaka chachiwiri, mwezi wachiwiri, pa tsiku la 20 la mweziwo,+ mtambo uja unanyamuka pamwamba pa chihema+ cha Umboni.