Numeri 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mtambowo ukanyamuka pamwamba pa chihemacho, Aisiraeli ankanyamuka nthawi yomweyo.+ Ndipo pamalo pamene mtambowo waima, mʼpamene Aisiraeli ankamangapo msasa.+ Salimo 78:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iye ankawatsogolera ndi mtambo masanaNdipo usiku wonse ankawatsogolera ndi kuwala kwa moto.+
17 Mtambowo ukanyamuka pamwamba pa chihemacho, Aisiraeli ankanyamuka nthawi yomweyo.+ Ndipo pamalo pamene mtambowo waima, mʼpamene Aisiraeli ankamangapo msasa.+