Numeri 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mtambowo ukanyamuka pamwamba pa chihemacho, ana a Isiraeli anali kunyamuka nthawi yomweyo.+ Ndipo pamalo pamene mtambowo waima, m’pamene ana a Isiraeli anali kumangapo msasa.+
17 Mtambowo ukanyamuka pamwamba pa chihemacho, ana a Isiraeli anali kunyamuka nthawi yomweyo.+ Ndipo pamalo pamene mtambowo waima, m’pamene ana a Isiraeli anali kumangapo msasa.+