Ekisodo 40:36, 37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Mʼzigawo zonse za ulendo wawo, mtambowo ukachoka pamwamba pa chihemacho nʼkukwera mʼmwamba, Aisiraeli ankanyamuka nʼkuyamba ulendo.+ 37 Koma ukapanda kukwera mʼmwamba, iwo sankanyamuka mpaka tsiku limene udzakwere.+
36 Mʼzigawo zonse za ulendo wawo, mtambowo ukachoka pamwamba pa chihemacho nʼkukwera mʼmwamba, Aisiraeli ankanyamuka nʼkuyamba ulendo.+ 37 Koma ukapanda kukwera mʼmwamba, iwo sankanyamuka mpaka tsiku limene udzakwere.+