Ekisodo 40:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 M’zigawo zonse za ulendo wawo, mtambowo ukakwera pamwamba pa chihema chokumanako, ana a Isiraeli anali kunyamuka n’kuyamba ulendo.+
36 M’zigawo zonse za ulendo wawo, mtambowo ukakwera pamwamba pa chihema chokumanako, ana a Isiraeli anali kunyamuka n’kuyamba ulendo.+