Numeri 10:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Akaliza malipenga onse awiriwo, gulu lonse lizibwera kwa iwe pakhomo la chihema chokumanako.+