Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 31:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndiyeno Mose anatumiza amunawo kunkhondo, amuna 1,000 pa fuko lililonse. Anawatumiza limodzi ndi Pinihasi,+ mwana wa wansembe Eleazara. Pinihasi ananyamula ziwiya zopatulika ndi malipenga operekera zizindikiro.+

  • 1 Mbiri 15:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Sebaniya, Yosafati, Netaneli, Amasai, Zekariya, Benaya ndi Eliezere, omwe anali ansembe, ankaimba malipenga mokweza patsogolo pa Likasa la Mulungu woona.+ Obedi-edomu ndi Yehiya nawonso anali alonda apageti panyumba yomwe munkakhala Likasa.

  • 1 Mbiri 16:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Benaya ndi Yahazieli, omwe anali ansembe, ankaimba malipenga nthawi zonse patsogolo pa likasa la pangano la Mulungu woona.

  • 2 Mbiri 29:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Choncho Aleviwo anaimirira atanyamula zipangizo zoimbira za Davide. Iwo anaimirira pamodzi ndi ansembe omwe ananyamula malipenga.+

  • Nehemiya 12:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Analinso ndi ena mwa ana a ansembe oimba malipenga:+ Zekariya mwana wa Yonatani. Yonatani anali mwana wa Semaya, Semaya anali mwana wa Mataniya, Mataniya anali mwana wa Mikaya, Mikaya anali mwana wa Zakuri ndipo Zakuri anali mwana wa Asafu.+

  • Nehemiya 12:41
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 41 Panafikanso ansembe otsatirawa okhala ndi malipenga: Eliyakimu, Maaseya, Miniyamini, Mikaya, Elioenai, Zekariya, Hananiya,

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena