Nehemiya 12:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Mwa ana a ansembe oimba malipenga+ panalinso Zekariya mwana wa Yonatani. Yonatani anali mwana wa Semaya, Semaya anali mwana wa Mataniya, Mataniya anali mwana wa Mikaya, Mikaya anali mwana wa Zakuri,+ ndipo Zakuri anali mwana wa Asafu.+
35 Mwa ana a ansembe oimba malipenga+ panalinso Zekariya mwana wa Yonatani. Yonatani anali mwana wa Semaya, Semaya anali mwana wa Mataniya, Mataniya anali mwana wa Mikaya, Mikaya anali mwana wa Zakuri,+ ndipo Zakuri anali mwana wa Asafu.+