Nehemiya 12:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Analinso ndi ena mwa ana a ansembe oimba malipenga:+ Zekariya mwana wa Yonatani. Yonatani anali mwana wa Semaya, Semaya anali mwana wa Mataniya, Mataniya anali mwana wa Mikaya, Mikaya anali mwana wa Zakuri ndipo Zakuri anali mwana wa Asafu.+
35 Analinso ndi ena mwa ana a ansembe oimba malipenga:+ Zekariya mwana wa Yonatani. Yonatani anali mwana wa Semaya, Semaya anali mwana wa Mataniya, Mataniya anali mwana wa Mikaya, Mikaya anali mwana wa Zakuri ndipo Zakuri anali mwana wa Asafu.+