Numeri 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mutenge amuna ena kuti akuthandizeni. Mutenge mwamuna mmodzi pafuko lililonse ndipo akhale mtsogoleri wa nyumba ya makolo ake.+ Numeri 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 kuchokera ku fuko la Dani, Ahiyezeri+ mwana wa Amisadai, Numeri 2:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Amene azimanga msasa wawo kumpoto ndi gulu la mafuko atatu la Dani ndi magulu awo.* Mtsogoleri wa ana a Dani ndi Ahiyezeri,+ mwana wa Amisadai. Numeri 2:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Asilikali onse a gulu la Dani amene analembedwa mayina alipo 157,600. Amenewa azikhala omalizira kunyamuka,+ mogwirizana ndi magulu a Aisiraeli a mafuko atatuatatu.”
4 Mutenge amuna ena kuti akuthandizeni. Mutenge mwamuna mmodzi pafuko lililonse ndipo akhale mtsogoleri wa nyumba ya makolo ake.+
25 Amene azimanga msasa wawo kumpoto ndi gulu la mafuko atatu la Dani ndi magulu awo.* Mtsogoleri wa ana a Dani ndi Ahiyezeri,+ mwana wa Amisadai.
31 Asilikali onse a gulu la Dani amene analembedwa mayina alipo 157,600. Amenewa azikhala omalizira kunyamuka,+ mogwirizana ndi magulu a Aisiraeli a mafuko atatuatatu.”