Numeri 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Aisiraeli onse anayamba kungʼungʼudzira Mose ndi Aroni,+ ndipo gulu lonselo linati: “Zikanakhala bwino tikanangofera ku Iguputo, kapena tikanangofera mʼchipululu muno. Numeri 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kodi ukuyesa nʼchinthu chachingʼono kuti unatichotsa mʼdziko loyenda mkaka ndi uchi kuti udzatiphere mʼchipululu muno?+ Kodi tsopano ukufunanso kuti wotilamulira ukhale iwe wekha? Numeri 16:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Koma tsiku lotsatira, gulu lonse la Aisiraeli linayamba kungʼungʼudza motsutsana ndi Mose komanso Aroni+ kuti: “Mwapha anthu a Yehova inu.”
2 Aisiraeli onse anayamba kungʼungʼudzira Mose ndi Aroni,+ ndipo gulu lonselo linati: “Zikanakhala bwino tikanangofera ku Iguputo, kapena tikanangofera mʼchipululu muno.
13 Kodi ukuyesa nʼchinthu chachingʼono kuti unatichotsa mʼdziko loyenda mkaka ndi uchi kuti udzatiphere mʼchipululu muno?+ Kodi tsopano ukufunanso kuti wotilamulira ukhale iwe wekha?
41 Koma tsiku lotsatira, gulu lonse la Aisiraeli linayamba kungʼungʼudza motsutsana ndi Mose komanso Aroni+ kuti: “Mwapha anthu a Yehova inu.”