Deuteronomo 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kumbukirani ndipo musamaiwale mmene munakwiyitsira Yehova Mulungu wanu mʼchipululu.+ Anthu inu mwakhala mukupandukira Yehova kuyambira tsiku limene munachoka mʼdziko la Iguputo mpaka kudzafika malo ano.+ Deuteronomo 31:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ineyo ndikudziwa bwino khalidwe lanu lopanduka+ ndi kuuma mtima* kwanu.+ Ngati mwakhala mukupandukira Yehova pamene ndili moyo, ndiye kuli bwanji pambuyo pa imfa yanga!
7 Kumbukirani ndipo musamaiwale mmene munakwiyitsira Yehova Mulungu wanu mʼchipululu.+ Anthu inu mwakhala mukupandukira Yehova kuyambira tsiku limene munachoka mʼdziko la Iguputo mpaka kudzafika malo ano.+
27 Ineyo ndikudziwa bwino khalidwe lanu lopanduka+ ndi kuuma mtima* kwanu.+ Ngati mwakhala mukupandukira Yehova pamene ndili moyo, ndiye kuli bwanji pambuyo pa imfa yanga!