-
Levitiko 27:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Ngati munthuyo ndi woyambira mwezi umodzi kufika zaka 5, akakhala wamwamuna mtengo wake womwe unaikidwa ndi masekeli asiliva 5, ndipo akakhala wamkazi ndi masekeli asiliva atatu.
-