Ekisodo 12:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Lamulo lililonse lizigwira ntchito mofanana kwa mbadwa ndi kwa mlendo wokhala pakati panu.”+ Levitiko 24:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chigamulo chilichonse chizigwira ntchito mofanana kwa mlendo wokhala pakati panu ndi kwa nzika,+ chifukwa ine ndine Yehova Mulungu wanu.’” Numeri 15:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Inu amene ndinu mpingo wa Isiraeli komanso mlendo amene akukhala pakati panu, mukhale ndi malamulo ofanana. Muzitsatira malamulo amenewa mʼmibadwo yanu yonse mpaka kalekale, mlendo komanso inuyo nʼchimodzimodzi pamaso pa Yehova.+
22 Chigamulo chilichonse chizigwira ntchito mofanana kwa mlendo wokhala pakati panu ndi kwa nzika,+ chifukwa ine ndine Yehova Mulungu wanu.’”
15 Inu amene ndinu mpingo wa Isiraeli komanso mlendo amene akukhala pakati panu, mukhale ndi malamulo ofanana. Muzitsatira malamulo amenewa mʼmibadwo yanu yonse mpaka kalekale, mlendo komanso inuyo nʼchimodzimodzi pamaso pa Yehova.+