Levitiko 22:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Uwauze kuti, ‘Mʼmibadwo yanu yonse munthu aliyense wodetsedwa mwa ana anu, amene wakhudza zinthu zopatulika zimene Aisiraeli azipatula kuti azipereke nsembe kwa Yehova, munthu ameneyo aziphedwa kuti asakhalenso pamaso panga.+ Ine ndine Yehova. Aheberi 10:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Munthu aliyense amene wanyalanyaza Chilamulo cha Mose amafa popanda kumuchitira chifundo, ngati anthu awiri kapena atatu apereka umboni.+
3 Uwauze kuti, ‘Mʼmibadwo yanu yonse munthu aliyense wodetsedwa mwa ana anu, amene wakhudza zinthu zopatulika zimene Aisiraeli azipatula kuti azipereke nsembe kwa Yehova, munthu ameneyo aziphedwa kuti asakhalenso pamaso panga.+ Ine ndine Yehova.
28 Munthu aliyense amene wanyalanyaza Chilamulo cha Mose amafa popanda kumuchitira chifundo, ngati anthu awiri kapena atatu apereka umboni.+