Ekisodo 16:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Aisiraeli ataona tinthu timeneti anayamba kufunsana kuti: “Nʼchiyani ichi?” chifukwa sankadziwa kuti chinali chiyani. Mose anawauza kuti: “Ndi chakudya chimene Yehova wakupatsani.+ Numeri 11:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma pano tilibe ndi mphamvu zomwe. Sitikuonanso chilichonse kupatulapo manawa.”+ Salimo 78:24, 25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Iye anapitiriza kuwagwetsera mana ngati mvula kuti adye.Anawapatsa tirigu wochokera kumwamba.+ 25 Anthu anadya chakudya cha amphamvu.*+Iye anawapatsa chakudya chokwanira.+
15 Aisiraeli ataona tinthu timeneti anayamba kufunsana kuti: “Nʼchiyani ichi?” chifukwa sankadziwa kuti chinali chiyani. Mose anawauza kuti: “Ndi chakudya chimene Yehova wakupatsani.+
24 Iye anapitiriza kuwagwetsera mana ngati mvula kuti adye.Anawapatsa tirigu wochokera kumwamba.+ 25 Anthu anadya chakudya cha amphamvu.*+Iye anawapatsa chakudya chokwanira.+