1 Akorinto 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Zinthu zimenezi ndi zitsanzo kwa ife, kuti nafenso tisamalakelake zinthu zoipa ngati mmene iwo anachitira.+ 1 Akorinto 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tisamamuyesenso Yehova,* mmene ena a iwo anamuyesera,+ nʼkufa atalumidwa ndi njoka.+
6 Zinthu zimenezi ndi zitsanzo kwa ife, kuti nafenso tisamalakelake zinthu zoipa ngati mmene iwo anachitira.+