-
Numeri 21:5, 6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Choncho iwo anayamba kudandaula motsutsana ndi Mulungu komanso Mose+ kuti: “Nʼchifukwa chiyani munatitulutsa mʼdziko la Iguputo kuti tidzafere mʼchipululu muno? Kuno kulibe chakudya komanso madzi,+ ndipo chakudya chonyansachi chafika potikola.”+ 6 Ndiyeno Yehova anatumiza njoka zapoizoni* pakati pawo, ndipo zinayamba kuwaluma moti Aisiraeli ambiri anafa.+
-