Salimo 46:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba ali ndi ife.+Mulungu wa Yakobo ndi malo athu othawirako otetezeka.+ (Selah) Salimo 91:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndidzauza Yehova kuti: “Inu ndinu malo anga othawirako komanso malo anga achitetezo,+Mulungu wanga amene ndimamukhulupirira.”+
11 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba ali ndi ife.+Mulungu wa Yakobo ndi malo athu othawirako otetezeka.+ (Selah)
2 Ndidzauza Yehova kuti: “Inu ndinu malo anga othawirako komanso malo anga achitetezo,+Mulungu wanga amene ndimamukhulupirira.”+