Salimo 91:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndidzauza Yehova kuti: “Inu ndinu pothawirapo panga ndi malo anga achitetezo,+Mulungu wanga amene ndimamukhulupirira.”+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 91:2 Nsanja ya Olonda,1/15/2010, ptsa. 9-1011/15/2001, tsa. 16
2 Ndidzauza Yehova kuti: “Inu ndinu pothawirapo panga ndi malo anga achitetezo,+Mulungu wanga amene ndimamukhulupirira.”+