Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 20:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Musalakelake nyumba ya mnzanu. Musalakelake mkazi wa mnzanu,+ kapolo wake wamwamuna, kapolo wake wamkazi, ngʼombe yake yamphongo, bulu wake, kapena chinthu chilichonse cha mnzanu.”+

  • Luka 12:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Kenako anauza anthuwo kuti: “Khalani maso ndipo chenjerani ndi dyera* lamtundu uliwonse,+ chifukwa ngakhale munthu atakhala ndi zochuluka chotani, moyo wake suchokera mʼzinthu zimene ali nazo.”+

  • Aroma 7:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndiye tinene kuti chiyani? Kodi Chilamulo ndi uchimo? Ayi ndithu. Kunena zoona, sindikanadziwa uchimo zikanakhala kuti panalibe Chilamulo.+ Mwachitsanzo, sindikanadziwa kusirira kwa nsanje zikanakhala kuti Chilamulo sichinanene kuti: “Usasirire mwansanje.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena