-
Deuteronomo 12:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Muzionetsetsa kuti mukumvera mawu onsewa amene ndikukuuzani, kuti nthawi zonse zinthu zizikuyenderani bwino, inuyo ndi ana anu obwera mʼmbuyo mwanu, chifukwa choti mukuchita zabwino ndi zoyenera pamaso pa Yehova Mulungu wanu.
-