Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 15:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Mphamvu ndi nyonga zanga ndi Ya,* chifukwa wandipulumutsa.+

      Ameneyu ndi Mulungu wanga ndipo ndidzamʼtamanda.+ Ndi Mulungu wa bambo anga,+ ndipo ndidzamulemekeza.+

  • Chivumbulutso 19:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Kenako ndinamva mawu amene ankamveka ngati mawu a khamu lalikulu, ngati mkokomo wa madzi ambiri komanso ngati mabingu amphamvu. Mawuwo anali akuti: “Tamandani Ya!*+ chifukwa Yehova* Mulungu wathu, Wamphamvuyonse,+ wayamba kulamulira monga mfumu!+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena