Chivumbulutso 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako ndinamva mawu ngati a khamu lalikulu, omveka ngati mkokomo wa madzi ambiri ndi mabingu amphamvu. Mawuwo anati: “Tamandani Ya,+ anthu inu, chifukwa Yehova* Mulungu wathu, Wamphamvuyonse,+ wayamba kulamulira monga mfumu.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:6 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 274-275 Nsanja ya Olonda,5/1/1993, ptsa. 25-2612/15/1990, tsa. 167/1/1989, ptsa. 23-24
6 Kenako ndinamva mawu ngati a khamu lalikulu, omveka ngati mkokomo wa madzi ambiri ndi mabingu amphamvu. Mawuwo anati: “Tamandani Ya,+ anthu inu, chifukwa Yehova* Mulungu wathu, Wamphamvuyonse,+ wayamba kulamulira monga mfumu.+
19:6 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 274-275 Nsanja ya Olonda,5/1/1993, ptsa. 25-2612/15/1990, tsa. 167/1/1989, ptsa. 23-24