Deuteronomo 17:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anthu onse adzamva zimenezo nʼkuchita mantha ndipo sadzachitanso zinthu modzikuza.+ 1 Timoteyo 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Anthu amene ali ndi chizolowezi chochita tchimo,+ uziwadzudzula+ pamaso pa onse kuti ena onsewo akhale ndi mantha.*
20 Anthu amene ali ndi chizolowezi chochita tchimo,+ uziwadzudzula+ pamaso pa onse kuti ena onsewo akhale ndi mantha.*