9 Kenako Mose analemba Chilamulo+ chimenechi nʼkuchipereka kwa ansembe, omwe ndi Alevi, amene amanyamula likasa la pangano la Yehova, komanso kwa akulu onse a Isiraeli.
8 Kenako Hilikiya mkulu wa ansembe anauza Safani mlembi+ kuti: “Ndapeza buku la Chilamulo+ mʼnyumba ya Yehova!” Choncho Hilikiya anapereka bukulo kwa Safani ndipo iye anayamba kuliwerenga.+