9 Nʼchifukwa chake fuko la Levi silinapatsidwe gawo kapena cholowa ngati abale awo. Cholowa chawo ndi Yehova, mogwirizana ndi zimene Yehova Mulungu wanu anawauza.+
14 Fuko la Levi lokha ndi limene sanalipatse malo monga cholowa chawo.+ Cholowa chawo ndi nsembe zotentha ndi moto zoperekedwa kwa Yehova Mulungu wa Isiraeli,+ mogwirizana ndi zimene anawalonjeza.+