1 Akorinto 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano abale, ndikufuna mudziwe kuti makolo athu akale, onse anali pansi pa mtambo+ ndipo onse anawoloka nyanja.+ 1 Akorinto 10:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ngakhale zinali choncho, ambiri a iwo Mulungu sanakondwere nawo ndipo anaphedwa mʼchipululu.+
10 Tsopano abale, ndikufuna mudziwe kuti makolo athu akale, onse anali pansi pa mtambo+ ndipo onse anawoloka nyanja.+