Genesis 46:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mulungu anamuuza kuti: “Ine ndine Mulungu woona, Mulungu wa bambo ako.+ Usaope kupita ku Iguputo, chifukwa kumeneko ndidzakupangitsa kukhala mtundu waukulu.+ Machitidwe 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno Yakobo anapita ku Iguputo+ kumene iye ndi makolo athu aja anafera.+
3 Mulungu anamuuza kuti: “Ine ndine Mulungu woona, Mulungu wa bambo ako.+ Usaope kupita ku Iguputo, chifukwa kumeneko ndidzakupangitsa kukhala mtundu waukulu.+