Machitidwe 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yakobo anapita ku Iguputo+ kumene iye ndi makolo athu+ aja anamwalirira.+