11 Chifukwa chakuti mumalamula anthu osauka kuti akulipireni akabwereka munda,
Ndipo mumatenga zokolola zawo ngati msonkho,+
Simudzapitiriza kukhala mʼnyumba zamiyala yosema zimene mwamanga.+
Ndiponso simudzamwa vinyo wochokera mʼminda yanu ya mpesa yabwino kwambiri.+