2 Mbiri 36:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho anawabweretsera mfumu ya Akasidi+ yomwe inapha anyamata awo ndi lupanga+ mʼnyumba yopatulika.+ Sinamvere chisoni mnyamata kapena namwali, wachikulire kapena wodwala.+ Mulungu anapereka zonse mʼmanja mwake.+ Yesaya 47:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ine ndinakwiyira anthu anga.+ Ndinalola kuti cholowa changa chidetsedwe+Ndipo ndinawapereka mʼmanja mwako.+ Koma iwe sunawachitire chifundo.+ Ngakhale munthu wokalamba unamusenzetsa goli lolemera kwambiri.+ Luka 19:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Iwo adzakugwetsa pansi nʼkukuwononga limodzi ndi ana ako amene ali mwa iwe.+ Ndipo sadzasiya mwala pamwamba pa mwala unzake mwa iwe,+ chifukwa sunazindikire kuti nthawi yokuyendera inali itakwana.”
17 Choncho anawabweretsera mfumu ya Akasidi+ yomwe inapha anyamata awo ndi lupanga+ mʼnyumba yopatulika.+ Sinamvere chisoni mnyamata kapena namwali, wachikulire kapena wodwala.+ Mulungu anapereka zonse mʼmanja mwake.+
6 Ine ndinakwiyira anthu anga.+ Ndinalola kuti cholowa changa chidetsedwe+Ndipo ndinawapereka mʼmanja mwako.+ Koma iwe sunawachitire chifundo.+ Ngakhale munthu wokalamba unamusenzetsa goli lolemera kwambiri.+
44 Iwo adzakugwetsa pansi nʼkukuwononga limodzi ndi ana ako amene ali mwa iwe.+ Ndipo sadzasiya mwala pamwamba pa mwala unzake mwa iwe,+ chifukwa sunazindikire kuti nthawi yokuyendera inali itakwana.”