Yoswa 19:1, 2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Maere achiwiri+ anagwera Simiyoni, kutanthauza fuko la Simiyoni,+ motsatira mabanja awo. Cholowa chawo chinali pakati pa cholowa cha Yuda.+ 2 Cholowa chawocho chinali Beere-seba+ kuphatikizapo Sheba, Molada,+
19 Maere achiwiri+ anagwera Simiyoni, kutanthauza fuko la Simiyoni,+ motsatira mabanja awo. Cholowa chawo chinali pakati pa cholowa cha Yuda.+ 2 Cholowa chawocho chinali Beere-seba+ kuphatikizapo Sheba, Molada,+