Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 21:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Nʼchifukwa chake malowo anawapatsa dzina lakuti Beere-seba,*+ chifukwa chakuti onse awiri analumbira pamalopo.

  • Genesis 26:32, 33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Tsiku limenelo, atumiki a Isaki anapita kwa iye nʼkumuuza zokhudza chitsime chimene anakumba.+ Anamuuza kuti: “Ife tapeza madzi.” 33 Choncho chitsimecho anachipatsa dzina lakuti Siba.* Nʼchifukwa chake dzina la mzindawo ndi Beere-seba+ mpaka lero.

  • Yoswa 15:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Mizinda ya kumapeto kwa gawo la fuko la Yuda, chakumalire ndi Edomu+ kumʼmwera, inali Kabizeeli, Ederi, Yaguri,

  • Yoswa 15:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Hazara-suali, Beere-seba,+ Bizioti,

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena