Genesis 21:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Nʼchifukwa chake malowo anawapatsa dzina lakuti Beere-seba,*+ chifukwa chakuti onse awiri analumbira pamalopo. Yoswa 19:1-3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Maere achiwiri+ anagwera Simiyoni, kutanthauza fuko la Simiyoni,+ motsatira mabanja awo. Cholowa chawo chinali pakati pa cholowa cha Yuda.+ 2 Cholowa chawocho chinali Beere-seba+ kuphatikizapo Sheba, Molada,+ 3 Hazara-suali,+ Bala, Ezemu,+
31 Nʼchifukwa chake malowo anawapatsa dzina lakuti Beere-seba,*+ chifukwa chakuti onse awiri analumbira pamalopo.
19 Maere achiwiri+ anagwera Simiyoni, kutanthauza fuko la Simiyoni,+ motsatira mabanja awo. Cholowa chawo chinali pakati pa cholowa cha Yuda.+ 2 Cholowa chawocho chinali Beere-seba+ kuphatikizapo Sheba, Molada,+ 3 Hazara-suali,+ Bala, Ezemu,+